NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA December 2017

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa January 29 mpaka February 25, 2018.

“Ndikudziwa Kuti Adzauka”

N’chiyani chimatitsimikizira kuti akufa adzauka?

“Ndili ndi Chiyembekezo mwa Mulungu”

N’chifukwa chiyani tinganene kuti nkhani ya kuuka kwa akufa ili m’gulu la mfundo zazikulu zimene Akhristu amakhulupirira?

Makolo, Thandizani Ana Anu Kupeza Nzeru Kuti Adzapulumuke

Makolo ambiri achikhristu amada nkhawa mwana wawo akakhala kuti akufuna kudzipereka kwa Mulungu ndi kubatizidwa. Kodi angathandize bwanji ana awo kuti adzapeze moyo wosatha?

Achinyamata, “Pitirizani Kukonza Chipulumutso Chanu”

Munthu akabatizidwa amakhala ndi udindo waukulu, koma achinyamata sayenera kuopa kapena kuzengereza kuti abatizidwe.