Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA Na. 2 2018 | Kodi M’tsogolomu Muli Zotani?

Kodi M’tsogolomu Muli Zotani?

Kodi munayamba mwadzifunsapo kuti tsogolo lanu komanso la banja lanu lidzakhala lotani? Baibulo limati:

“Olungama adzalandira dziko lapansi, ndipo adzakhala mmenemo kwamuyaya.”​—Salimo 37:29.

Nsanja ya Olonda iyi ikuthandizani kudziwa cholinga cha Mulungu kwa anthu komanso dzikoli. Ikufotokozanso zimene mungachite kuti mudzasangalale cholingachi chikadzakwaniritsidwa.

 

Kodi Pali Amene Angadziwiretu Zam’tsogolo?

Anthu akhala akuneneratu zinthu zomwe zidzachitike zaka masauzande ambiri m’tsogolo ndipo zina zimachitika pamene zina sizichitika n’komwe.

Kodi Okhulupirira Nyenyezi Komanso Olosera Angatithandizedi Kudziwa Zam’tsogolo?

Kodi muyenera kudalira anthu okhulupirira nyenyezi kuti akuthandizeni kudziwa zam’tsogolo?

Maulosi Amene Anakwaniritsidwa

Maulosi a m’Babulo amakwaniritsidwa mochititsa chidwi kwambiri.

Chipilala Chomwe Chimasonyeza Kuti Maulosi a M’Baibulo Ndi Olondola

Chipilala chakale kwambiri chomwe chimasonyeza kuti maulosi a m’Baibulo ndi olondola.

Malonjezo Amene Adzakwaniritsidwe

Maulosi a m’Baibulo ambirimbiri anakwaniritsidwa ndipo tikuyembekezera kuti ena adzakwaniritsidwa m’tsogolomu.

Mukhoza Kudzakhala Padzikoli Kwamuyaya

Baibulo limafotokoza cholinga chimene Mlengi ali nacho chokhudza anthu.

Tsogolo Lanu Lili M’manja Mwanu

Anthu ambiri amakhulupirira kuti Mulungu analemberatu tsogolo lawo. Koma kodi zimenezi ndi zoona?

“Anthu Ofatsa Adzalandira Dziko Lapansi”

Baibulo limalonjeza kuti idzafika nthawi pamene sikudzakhalanso zoipa ndiponso zinthu zopanda chilungamo.