NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA August 2018

Magazini ino ili na nkhani zophunzila wiki ya October 1-28, 2018.

Kodi Mudziŵa Bwino Zoona Zake?

Ni mfundo zitatu ziti za m’Baibo zimene zingatithandize kupenda mosamala zimene tamvela kuti tidziŵe ngati n’zoona?

Musamaweluze Poona Maonekedwe Akunja

Onani mbali zitatu zimene zionetsa kuti kuweluza ena poona maonekedwe awo akunja si cinthu canzelu.

MBILI YANGA

N’natsimikiza Mtima Kuti Sinidzabwelela M’mbuyo

Mvelani zocitika zimene m’bale Maxim Danyleyko wasangalala nazo m’zaka 68 zimene watumikila monga mmishonale.

Opatsa Mowoloŵa Manja Amakhala Acimwemwe

Kodi kukhala owolowa manja kumatithandiza bwanji kukhala acimwemwe?

Muziseŵenza na Yehova Tsiku Lililonse

Kodi tingaseŵenze na Yehova m’njila 5 ziti?

Kuleza mtima Kumatanthauza Kupilila Tili na Colinga

Phunzilani zimene kuleza mtima kumatanthauza, mmene tingakulitsile khalidweli, na mapindu amene tingapeze tikakhala oleza mtima

ZA M'NKHOKWE YATHU

Kufesa Mbewu za Ufumu ku Portugal

Ni mavuto anji amene alaliki a Ufumu oyambilila ku Portugal anakumana nawo?