NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) December 2018

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa February 4 mpaka March 3, 2019.

“Tidzaonana M’Paradaiso”

Kodi mawu oti paradaiso amatanthauza chiyani kwa inuyo? Kodi mukuyembekezera kudzakhala m’paradaiso?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi mawu oti “kumwamba kwachitatu” opezeka pa 2 Akorinto 12:2 akutanthauza chiyani?

Kodi Mukukumbukira?

Kodi mwawerenga magazini aposachedwapa a Nsanja ya Olonda? Onani zimene mungakumbukire.

Tizilemekeza “Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi”

Kodi Malemba amanena kuti munthu angathetse banja n’kukwatiranso pa chifukwa chiti?

‘Yehova Watichitira Zinthu Zabwino’

Werenga mbiri ya moyo wa Jean-Marie Bockaert, yemwe anatumikira ku ofesi ya nthambi ya ku France limodzi ndi mkazi wake dzina lake Danièle kwa zaka zoposa 50.

Achinyamata, Mlengi Wanu Amafuna Kuti Muzikhala Osangalala

Kodi ndi zinthu 4 ziti zimene zingathandize wachinyamata kukhala ndi moyo wosangalala komanso tsogolo labwino?

Achinyamata, Mukhoza Kukhala ndi Moyo Wosangalala

Kodi mawu a mu Salimo 16 angathandize bwanji achinyamata kuti akhale ndi moyo wosangalala panopa komanso m’tsogolo?

“Wolungama adzakondwera mwa Yehova”

Kodi tingatani kuti tizikhalabe osangalala ngakhale tikumane ndi mavuto?

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2018

Mlozera nkhani wa nkhani zonse za m’magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! a 2018.