NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA December 2018

Magazini ino ili na nkhani zophunzila wiki ya February 4-March 3, 2019.

“Tidzaonana M’Paradaiso!”

Kodi mumaganiza kuti Paradaiso n’ciani? Kodi mumakhulupilila kuti idzakhalakodi?

Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga

Kodi “kumwamba kwacitatu” kochulidwa pa 2 Akorinto 12:2 n’ciani?

Kodi Mukumbukila?

Kodi munaŵelenga na kumvetsetsa mfundo za m’magazini aposacedwa a Nsanja ya Mlonda? Ngati n’conco, ni mafunso angati ozikidwa pa Baibo amene mungakwanitse kuyankha?

Muzilemekeza “Cimene Mulungu Wacimanga Pamodzi”

Kodi ni maziko okha ati a m’Malemba acisudzulo?

‘Yehova Waticitila Zinthu Zabwino’

Ŵelengani nkhani yofotokoza za umoyo wa m’bale Jean-Marie Bockaert, amene anatumikila na mkazi wake, Danièle, pa ofesi ya nthambi ku France, kwa zaka zoposa 50.

Acicepele, Mlengi Wanu Amafuna Kuti Mukhale Acimwemwe

N’zinthu zinayi ziti zimene zingathandize wacicepele kukhala na umoyo wacimwemwe komanso wopambana?

Acicepele, Mungakhale na Umoyo Wacimwemwe

Kodi mfundo za mu Salimo 16 zingathandize bwanji acicepele kukhala na umoyo wacimwemwe tsopano komanso kutsogolo?

“Wolungama Adzakondwela mwa Yehova”

N’ciani cingatithandize kukhalabe acimwemwe ngakhale tikukumana na mavuto?

Mlongoza Nkhani wa Magazini a 2018 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!

Mlongoza nkhani wokhala na nkhani zonse za m’magazini a 2018 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka! zondandalikidwa potengela mitu.