NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA December 2018

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa February 4 mpaka March 3, 2019.

“Tidzaonana M’Paradaiso”

Kodi mawu oti paradaiso amatanthauza chiyani kwa inuyo? Kodi mukuyembekezera kudzakhala m’paradaiso?

Tizilemekeza “Chimene Mulungu Wachimanga Pamodzi”

Kodi Malemba amanena kuti munthu angathetse banja n’kukwatiranso pa chifukwa chiti?

Achinyamata, Mlengi Wanu Amafuna Kuti Muzikhala Osangalala

Kodi ndi zinthu 4 ziti zimene zingathandize wachinyamata kukhala ndi moyo wosangalala komanso tsogolo labwino?

Achinyamata, Mukhoza Kukhala ndi Moyo Wosangalala

Kodi mawu a mu Salimo 16 angathandize bwanji achinyamata kuti akhale ndi moyo wosangalala panopa komanso m’tsogolo?