NSANJA YA OLONDA—YOPHUNZIRA February 2019

Pitirizani Kukhala ndi Mtima Wosagawanika

Kodi kukhala ndi mtima wosagawanika n’kutani nanga tingatani kuti tipitirize kukhala ndi khalidweli?

Yesetsani Kukhala Ofatsa Kuti Muzisangalatsa Yehova

Kodi Yesu ndi Mose anapereka chitsanzo chotani pa nkhani yokhala ofatsa? Kodi kukhala ofatsa n’kothandiza bwanji masiku ano?

Tizisonyeza Kuti Ndife Oyamikira

Kodi tingaphunzire chiyani kwa Yehova, Yesu ndi Msamaliya wakhate pa nkhani yosonyeza kuyamikira?

Aisiraeli Ankafunika Kusonyeza Chikondi ndi Chilungamo

Kodi Chilamulo cha Mose chimasonyeza chiyani pa mmene Yehova amaonera chikondi komanso chilungamo?