NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) March 2020

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira pa May 4-31, 2020.

Munthu Amabatizidwa Chifukwa Chokonda Yehova Komanso Kumuyamikira

Munthu amafuna kubatizidwa akayamba kukonda kwambiri Yehova. Koma kodi n’chiyani chingamulepheretse kuchita zimenezi?

Kodi Ndinu Okonzeka Kubatizidwa?

Zimene mungayankhe pa mafunso amunkhaniyi zingakuthandizeni kudziwa ngati mwakonzeka kubatizidwa kapena ayi.

MBIRI YA MOYO WANGA

“Ife tilipo. Titumizeni”

Jack ndi Marie-Line akufotokoza zimene zinawalimbikitsa kuti ayambe utumiki wa nthawi zonse komanso zimene zinkawathandiza kuzolowera zinthu zatsopano utumiki wawo ukasintha.

Kodi Mumadziwa Nthawi Yoyenera Kulankhula?

Onani zitsanzo za m’Baibulo zotithandiza kudziwa nthawi yoyenera kulankhula ndi yoyenera kukhala chete.

Muzikondana Kwambiri

Yesu ananena kuti chikondi ndi chizindikiro cha Akhristu oona. Kodi chikondi chimatithandiza bwanji kukhala mwamtendere ndi ena, opanda tsankho komanso ochereza?

Kodi Mukudziwa?

Kuwonjezera pa zimene Baibulo limanena, kodi pali umboni wina wosonyeza kuti Aisiraeli anali akapolo ku Iguputo?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi apolisi apakachisi anali ndani, nanga ntchito yawo inali yotani?