NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) December 2020

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira February 1-28, 2021.

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi mawu a Paulo opezeka pa 1 Akorinto 15:29, akutanthauza kuti Akhristu ena kalelo ankabatizidwa m’malo mwa anthu akufa?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Lemba la Miyambo 24:16 limati: “Wolungama akhoza kugwa ngakhale nthawi 7 ndipo ndithu adzadzukanso.” Kodi pamenepa akunena za munthu amene amachita machimo mobwerezabwereza koma kenako Mulungu n’kumukhululukira?