NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA December 2020
Magazini ino ili na nkhani zophunzila kuyambila pa February 1-28, 2021.
Mafunso Ocokela Kwa Oŵelenga
Kodi mawu a mtumwi Paulo pa 1 Akorinto 15:29 atanthauza kuti Akhristu ena m’nthawi yakale anali kubatizika cifukwa ca akufa?
Mafunso Ocokela Kwa Oŵelenga
Miyambo 24:16 imati : “Wolungama akhoza kugwa ngakhale nthawi 7 ndipo ndithu adzadzukanso.” Kodi lembali limakamba za munthu amene amagwela m’chimo mobweleza-bweleza koma Mulungu n’kumamukhululukila?