NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA December 2021

Magazini ino ili na nkhani zophunzila kuyambila pa January 31–February 27, 2022.

NKHANI YOPHUNZILA 48

“Muzikhala Oyela”

Kodi Mukukumbukila?

Kodi munapindula kuŵelenga magazini a Nsanja ya Mlonda a posacedwa? Onani ngati mukukumbukila.

NKHANI YOPHUNZILA 51

Pitilizani ‘Kumumvela’

Mlozela Nkhani wa Magazini a 2021 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!

Mlozela nkhani zonse zotulutsidwa m’magazini a 2021 a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!, zondandalikidwa potengela mitu.