NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA February 2022

Magazini ino ili na nkhani zophunzila kuyambila pa April 4–May 1, 2022

MBILI YANGA

N’napeza Cinthu Cabwino Kuposa Kukhala Dokotala

Mbili yanga: René Ruhlmann

Kodi Mudziŵa?

N’cifukwa ciani Aisiraeli kalelo anali kupeleka malipilo a ukwati?

Kodi Mudziŵa?

N’cifukwa ciani ana a nkhunda komanso njiŵa zinali kulandilidwa monga nsembe?