NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA September 2022

Magazini ino ili na nkhani zophunzila kuyambila pa November 7–December 4, 2022.

Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga

Ndani adzaukitsidwa pano padziko lapansi? Nanga ciukitso cawo cidzakhala cotani?

Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga

Kodi mtumwi Paulo anatanthauza ciyani pamene anati iye ni “khanda lobadwa masiku asanakwane”? (1 Akorinto 15:8)

MBILI YANGA

Nakhala Nikusangalala Kuphunzila za Yehova na Kuphunzitsako Ena

Mbili Yankho: M’bale Leon Weaver, Jr.