NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) August 2023

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira October 9–November 5, 2023.

NKHANI YOPHUNZIRA 33

Muziphunzira pa Chitsanzo cha Danieli

Idzaphunziridwa mlungu woyambira October 9-15, 2023

NKHANI YOPHUNZIRA 34

Muziphunzira Maulosi a M’Baibulo

Idzaphunziridwa mlungu wa October 16-22, 2023.

Ngati Mwamuna Kapena Mkazi Wanu Amaonera Zolaula

Kodi mwamuna ndi mkazi wake angatani kuti ayambirenso kukhulupirirana komanso kuti azithandizana ngati wina ali ndi vuto loonera zolaula?

NKHANI YOPHUNZIRA 35

Pitirizani Kukhala Oleza Mtima

Idzaphunziridwa mlungu wa October 23-29, 2023.

NKHANI YOPHUNZIRA 36

Nyamulani Zinthu Zofunika Ndipo Tayani Zina Zonse

Idzaphunziridwa mlungu wa October 30–November 5, 2023.