NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA August 2023

Magazini ino ili na nkhani zophunzila kuyambila pa October 9–November 5, 2023.

NKHANI YOPHUNZILA 33

Tengelani Citsanzo ca Danieli

Yophunzila mu mlungu wa October 9-15, 2023

NKHANI YOPHUNZILA 34

Phunzilani ku Maulosi a m’Baibo

Yophunzila mu mlungu wa October 16-22, 2023.

Ngati Mnzanu wa mu Ukwati Amaonelela Zamalisece

Kodi okwatilana angaseŵenzele bwanji pamodzi kuti athandize amene ali na vuto loonelela zamalisece, komanso kuti ayambilenso kukhulupililana?

NKHANI YOPHUNZILA 35

Khalanibe Oleza Mtima

Yophunzila mu mlungu wa October 23-29, 2023

NKHANI YOPHUNZILA 36

Nyamulani Zofunikila Zokhazo, Tayani Zotsalazo

Yophunzila mu mlungu wa October 30–November 5, 2023.