NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA October 2023

Magazini ino ili na nkhani zophunzila kuyambila pa December 11, 2023–January 7, 2024.

1923​—Zaka 100 Zapitazo

Caka a 1923 cinali colimbikitsa kwa Ophunzila Baibo pamene kulambila kwawo, na nchito yolalikila inaonetsa m’gwilizano umene umadziŵikitsa kulambila koona masiku ano.

NKHANI YOPHUNZILA 42

Kodi Ndinu ‘Wokonzeka Kumvela’?

Yophunzila mu mlungu wa December 11-17, 2023.

NKHANI YOPHUNZILA 43

Mulungu ‘Adzakupatsani Mphamvu’​—Motani?

Yophunzila mu mlungu wa December 18-24, 2023.

NKHANI YOPHUNZILA 44

Yesetsani Kumvetsa Milingo Yonse ya Mawu a Mulungu

Yophunzila mu mlungu wa December 25-31, 2023.

NKHANI YOPHUNZILA 45

Yamikilani Mwayi Wanu Wolambila Yehova M’kacisi Wake Wauzimu

Yophunzila mu mlungu wa January 1-7, 2024.