Onani zimene zilipo

Kukumbukila Imfa ya Yesu

Kukumbukila Imfa ya Yesu

Caka ciliconse, Mboni za Yehova zimakumbukila imfa ya Yesu mogwilizana ndi zimene iye anatilamula. (Luka 22:19, 20) Tikupemphani nonse kuti mudzapezeke pa cocitika cofunika kwambili cimeneci. Tidzaphunzila mmene tingapindulile ndi moyo wa Yesu ndiponso imfa yake.