Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2018
Pulogalamu ya 2018 “Limbani Mtima.” Msonkhano Wachigawo wa Mboni za Yehova.
Lachisanu
Pulogalamu ya tsiku limeneli yachokera pa Yoswa 1:7—“Khala wolimba mtima kwambiri ndipo uchite zinthu mwamphamvu.”
Loweruka
Kodi tingatani kuti tizilankhula mawu a Mulungu mopanda mantha?
Lamlungu
Pali zinthu zina zomwe zichitike m’tsogolomu, ndipo anthu a Mulungu adzafunika kukhala olimba mtima.
Mawu kwa Osonkhana
Dziwani zoyenera kuchita pa msonkhano wachigawo.