Buku Lothandiza Pophunzila Mau a Mulungu

Dzina la Mulungu m’Malemba a Ciheberi

N’cifukwa ciani Baibulo la dziko la tsopano limagwilitsila nchito dzina lakuti “Yehova” pamene Mabaibulo ena anacotsa dzina limeneli?

Dzina la Mulungu m’Malemba Acikristu Acigiriki

Onani maumboni otsimikizila kuti dzina la Mulungu likupezeka m’mipukutu yoyambilila ya Cigiriki

Chati: Aneneli ndi Mafumu a Yuda ndi a Isiraeli (Mbali 1)

Onani mbili ya m’Baibulo kucokela mu 997 B.C.E. mpaka mu 800 B.C.E.

Chati: Aneneli ndi Mafumu a Yuda ndi a Isiraeli (Mbali 2)

Onani mbili ya m’Baibulo kucokela mu 800 B.C.E. mpaka mu 607 B.C.E.

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Zocitika Zotifikitsa pa Nthawi ya Utumiki wa Yesu

Onani chati ndi mapu oonetsa zocitika kucokela mu 3 B.C.E. mpaka mu 29 C.E.

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Ciyambi ca Utumiki wa Yesu

Onani chati ndi mapu kucokela mu 29 C.E. mpaka pa Pasika wa mu 30 C.E.

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Utumiki Waukulu wa Yesu m’Galileya (Mbali 1)

Onani chati ndi mapu oonetsa nthawi kucokela mu 30 C.E. mpaka pa Pasika wa mu 31 C.E.

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Utumiki Waukulu wa Yesu m’Galileya (Mbali 2)

Onani chati ndi mapu oonetsa nthawi kucokela mu 31 C.E. mpaka pambuyo pa Pasika wa mu 32 C.E.

Zocitika zazikulu za paumoyo wa Yesu Padziko​—Utumiki wa Yesu ku Galileya (Mbali 3) ku Yudeya

Onani chati coonetsa nthawi kucokela mu 32 C.E. mpaka pakati pacikondwelelo ca Pasika ndi ca kupeleka kacisi

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko—Utumiki wa Yesu Wakumapeto Kum’maŵa kwa Yorodano

Onani mapu oonetsa nthawi kucokela mu 32 C.E. mpaka pambuyo pa cikondwelelo ca kupeleka kacisi.

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko​—Utumiki Womaliza wa Yesu m’Yerusalemu (Mbali 1)

Onani mapu oonetsa nthawi kucokela pa Nisani 8 mpaka pa Nisani 14, mu 33 C.E.

Zocitika Zazikulu Paumoyo wa Yesu wa Padziko—Utumiki Womaliza wa Yesu m’Yerusalemu (Mbali 2)

Onani mapu oonetsa nthawi kucokela pa Nisani 14 mpaka Iyara 25, mu 33 C.E.

Uthenga wa m’Baibulo

Baibulo ili ndi uthenga umodzi wosavuta kumva kucokela Genesis mpaka Chivumbulutso. Ndi uthenga wotani?

Buku la Genesis ndi Maulendo a Makolo Akale

Onani mapu m’buku la Genesis.

Kucoka ku Iguputo

Onani njila zimene Aisiraeli anayendemo popita ku dziko lolonjezedwa.

Kugonjetsa Dziko Lolonjezedwa

Onani mapu a nkhondo ya Aisiraeli.

Cihema ndi Mkulu wa Nsembe

Onani cithunzi ca cihema ndi zovala za ansembe aciisraeli.

Kukhala M’dziko Lolonjezedwa

Onani mapu a magawo ogaŵilidwa ku mafuko a Aisiraeli ndi a malo amene oweluza kucokela pa Otiniyeli mpaka pa Samsoni.

Ufumu wa Davide ndi wa Solomo

Onani mapu a fuko la Isiraeli pacimake.

Kacisi Amene Solomo Anamanga

Onani mbali zikuluzikulu 14 za maonekedwe akacisi.

Maulamulilo Amphamvu Padziko Onenedwelatu ndi Danieli

Onani cifanizilo cocititsa mantha ca pa Danieli caputala 2 ndiponso kukwanilitsidwa kwake.

Isiraeli m’Nthawi ya Yesu

Onani zigawo za Roma kuzungulila Isiraeli.WEB:OnSiteAdTitleIsiraeli m’Nthawi ya Yesu.

Kacisi Womangidwa pa Phili m’Zaka 100 Zoyambilila

Onani mbali zikuluzikulu za kacisi wa m’nthawi ya Yesu.

Mlungu Womaliza wa Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Mbali 1)

Onani mapu a Yerusalemu ndi malo ake ozungulila, ndiponso zimene zinacitika pa Nisani 8 mpaka 11 m’caka ca 33 C.E.

Mlungu Womaliza wa Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Mbali 2)

Onani mapu oonetsa nthawi kucokela pa Nisani 12 mpaka Nisani 16, mu 33 C.E.

Kufalikila kwa Cikristu

Onani mapu oonetsa maulendo a Paulo pofalitsa uthenga wabwino ndi mizinda yochulidwa m’buku la Chivumbulutso.

Malonda ndi Citukuko

Onani zithunzi zoonetsa muyezo wa zinthu za zamadzi, zimene si zamadzi, ndi miyezo ya mtunda zochulidwa m’Baibulo.

Ndalama ndi Muyezo

Onani zithunzi zoonetsa ndalama ndi muyezo wa zinthu zolemela zochulidwa m’Baibulo.

Kalendala ya Ciheberi

Yelekezelani kalendala ya miyezi ya m’Baibulo ndi kalendala ya miyezi ya masiku ano, ndipo onani nthawi ya zocitika m’caka conse