Nkhani Zina

Pamalowa mungapezepo nkhani zosiyanasiyana kuphatikizapo zomwe zili patsamba loyamba la jw.org. Werengani nkhani zimenezi komanso kuonera mavidiyo omwe alipo kuti mupeze nzeru zothandiza za m’Baibulo kuti mulimbitse chikhulupiriro chanu.

KHALANI MASO

Kodi Aramagedo Idzayambira ku Isiraeli?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Tingapeze yankho tikaona zomwe buku la Chivumbulutso limanena zokhudza Aramagedo.

Kodi Choonadi Ndi Chofunikabe Masiku Ano?

Baibulo lingakuthandizeni kudziwa choonadi m’dziko lomwe anthu ambiri akumafalitsa mabodza.

NTCHITO YAPADERA YOLALIKIRA

Nkhondo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Ufumu wa Mulungu udzachite kuti ubweretse mtendere weniweni komanso chitetezo.

KHALANI MASO

Katswiri wa za Umoyo Wachenjeza Kuti Achinyamata Angakumane Ndi Mavuto Pamalo Ochezera a pa Intaneti—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Onani mfundo za m’Baibulo zitatu zimene zingathandize makolo kuteteza ana awo.

KHALANI MASO

Nkhondo ya ku Ukraine Ikulowa Chaka Chachiwiri—Kodi Baibulo Limapereka Chiyembekezo Chotani?

Phunzirani zokhudza lonjezo lopezeka m’Baibulo lakuti nkhondo zonse zidzatha.

KHALANI MASO

Achinyamata Ambiri Akuvutika Ndi Matenda Amaganizo—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Baibulo limapereka malangizo othandiza kwa achinyamata omwe akuvutika maganizo.

KHALANI MASO

Ku Turkey ndi ku Syria Kwachitika Zivomerezi Zoopsa—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Anthu amene akhudzidwa ndi zivomerezi ku Turkey ndi ku Syria angalimbikitsidwe ndi kutonthozedwa ndi zimene Baibulo limanena.

KHALANI MASO

Asayansi Asunthira Kutsogolo Wotchi Yosonyeza Nthawi ya Kutha kwa Dziko—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Ngakhale kuti Baibulo limanena za mapeto, komabe limatithandizanso kukhala ndi maganizo oyenerera.

KHALANI MASO

Yambani Chaka cha 2023 Muli Ndi Chiyembekezo—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Anthu ambiri amakhala ndi chiyembekezo cha tsogolo lowala akangolowa m’chaka chatsopano. Uthenga wabwino wa m’Baibulo ungatithandize kukhala ndi tsogolo lowala.

KHALANI MASO

Kuwombera M’masukulu—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

N’chifukwa chiyani zinthu zoopsazi zimachitika? Kodi zinthu zachiwawa ngati zimenezi zingadzathedi?

KHALANI MASO

Anthu Ambirimbiri Athawa Nkhondo M’dziko la Ukraine

Baibulo limafotokoza zifukwa zenizeni zomwe zachititsa vutoli komanso mmene mavutowa adzathere mpaka kalekale.

Asilikari a Dziko la Russia Alowa M’dziko la Ukraine

Ngati ndi choncho, kodi Baibulo limafotokoza mmene zimenezi zithere?

Zimene Mungachite Mukaferedwa

Muone zinthu zimene zingakuthandizeni kupirira.

Zimene Mungachite Ngati Muli Nokhanokha

Mukamamva kuti muli nokhanokha, mungayambe kuona kuti simungathe kupeza chiyembekezo, chimwemwe komanso kukhala wokhutira​—komatu si choncho.

TSAMBA LOYAMBA

Kodi Choonadi Ndi Chofunikabe Masiku Ano?

Baibulo lingakuthandizeni kudziwa choonadi m’dziko lomwe anthu ambiri akumafalitsa mabodza.

NTCHITO YAPADERA YOLALIKIRA

Nkhondo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Ufumu wa Mulungu udzachite kuti ubweretse mtendere weniweni komanso chitetezo.

Zimene Mungachite Ngati Muli Nokhanokha

Mukamamva kuti muli nokhanokha, mungayambe kuona kuti simungathe kupeza chiyembekezo, chimwemwe komanso kukhala wokhutira​—komatu si choncho.

NKHANI ZOSIYANASIYANA

Zimene Mungachite Mukaferedwa

Muone zinthu zimene zingakuthandizeni kupirira.

Pepani, palibe mawu ofanana ndi omwe mwasankha.