Phunzilani kwa Mabwenzi a Yehova
Phunzilani kwa anthu osiyanasiyana ochulidwa m’Baibulo amene anakhala mabwenzi a Yehova!
Yeremiya
Kodi mungaphunzile ciyani kwa Yeremiya amene anali bwenzi la Yehova pa nkhani ya kukhala wolimba mtima?
Hananiya, Misayeli, ndi Azariya
Kodi mungakhale omvela monga mabwenzi a Yehova awa, Hananiya, Misayeli, ndi Azariya?
Pepani, palibe mawu olingana amene mwasankha.