DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Nyimbo ya Solomo Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 Buku la Ezara Machaputala 1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 Mitu 1 Mfumu Koresi inalamula kuti kachisi amangidwenso (1-4) Kukonzekera kuchoka ku ukapolo ku Babulo (5-11) 2 Anthu amene anabwerera kuchokera ku ukapolo (1-67) Atumiki a pakachisi (43-54) Ana a atumiki a Solomo (55-57) Zopereka zaufulu pakachisi (68-70) 3 Anamanganso guwa nʼkuperekapo nsembe (1-6) Ntchito yomanganso kachisi inayambika (7-9) Anamanga maziko a kachisi (10-13) 4 Anthu ankatsutsa ntchito yomanganso kachisi (1-6) Adani analemba kalata kwa Mfumu Aritasasita (7-16) Zomwe Aritasasita anayankha (17-22) Ntchito yomanga kachisi inaimitsidwa (23, 24) 5 Ayuda anayambiranso kumanga kachisi (1-5) Tatenai analembera kalata Mfumu Dariyo (6-17) 6 Dariyo anafufuza nʼkupereka lamulo (1-12) Kachisi anamalizidwa nʼkutseguliridwa (13-18) Anachita Pasika (19-22) 7 Ezara anapita ku Yerusalemu (1-10) Aritasasita analembera Ezara kalata (11-26) Ezara anatamanda Yehova (27, 28) 8 Anthu amene anabwerera ndi Ezara (1-14) Kukonzekera ulendo (15-30) Kunyamuka ku Babulo nʼkufika ku Yerusalemu (31-36) 9 Aisiraeli anakwatira akazi a mitundu ina (1-4) Pemphero la Ezara lovomereza machimo (5-15) 10 Pangano loti achotse akazi a mitundu ina (1-14) Akazi a mitundu ina anatumizidwa kwawo (15-44) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Ezara—Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) Ezara—Zimene Zili Mʼbukuli Chichewa Ezara—Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt Ezra p. 799