April 10-16
YEREMIYA 22-24
Nyimbo Na. 52 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Muli ndi ‘Mtima Wodziwa’ Yehova?”: (10 min.)
Yer. 24:1-3—Yehova anayerekezera anthu ndi nkhuyu (w13 3/15 8 ¶2)
Yer. 24:4-7—Nkhuyu zabwino zinkaimira anthu omwe anali ndi mtima womvera (w13 3/15 8 ¶4)
Yer. 24:8-10—Nkhuyu zoipa zinkaimira anthu a mtima wopanduka ndi wosamvera (w13 3/15 8 ¶3)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Yer. 22:30—Kodi lamuloli likusonyeza kuti Yesu sanali woyenera kukhala pa mpando wachifumu wa Davide? (w07 3/15 10 ¶9)
Yer. 23:33—Kodi “katundu wa Yehova” n’chiyani? (w07 3/15 11 ¶1)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yer 23:25-36
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g17.2 tsamba loyamba—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g17.2 tsamba loyamba—Muuzeni nkhani imene mudzakambirane ulendo wotsatira.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 5 ¶1-2—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 60
“Mungathe Kulimbikitsa Mkhristu Amene Anafooka”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Muzilimbikitsa Amene Anafooka.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 21 ¶13-22, komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 186
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 93 ndi Pemphero