Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

April 2-8

MATEYU 26

April 2-8

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Kufanana Komanso Kusiyana Komwe Kulipo Pakati pa Mwambo wa Pasika ndi Chikumbutso”: (10 min.)

    • Mat. 26:17-20​—Yesu anadya Pasika womaliza ndi atumwi ake (“Mwambo wa Pasika” zithunzi ndi mavidiyo mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 26:17-20, nwtsty)

    • Mat. 26:26​—Mkate wa pa Chikumbutso umaimira thupi la Yesu (“ukuimira” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 26:26, nwtsty)

    • Mat. 26:27, 28​—Vinyo amaimira ‘magazi ake a pangano’ (“magazi a pangano” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 26:27, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Mat. 26:17​—N’chifukwa chiyani tinganene kuti Nisani 13 linali “tsiku loyamba la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa”? (“Pa tsiku loyamba la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 26:17, nwtsty)

    • Mat. 26:39​—Kodi chiyenera kuti n’chiyani chinachititsa Yesu kupemphera kuti: “Kapu iyi indipitirire”? (“kapu iyi indipitirire“ mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 26:39, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 26:1-19

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 20

  • Zofunika Pampingo: (8 min.)

  • Khalani Bwenzi la Yehova​—Dipo: (7 min.) Onerani vidiyoyi. Kenako pemphani ana amene munawasankhiratu kuti abwere kupulatifomu ndipo muwafunse mafunso otsatirawa: Kodi n’chifukwa chiyani timadwala, kukalamba komanso kufa? Kodi Yehova anatipatsa chiyembekezo chotani? Kodi ndi ndani amene umafuna utadzamuona m’Paradaiso?

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 16 ¶1-5 komanso tsamba 168-169, 175, 176-177

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 74 ndi Pemphero