Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

April 23-29

MALIKO 3-4

April 23-29

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Anachiritsa Munthu pa Tsiku la Sabata”: (10 min.)

    • Maliko 3:1, 2​—Atsogoleri achipembedzo achiyuda ankafuna kumupezera Yesu chifukwa chomuimbira mlandu (jy 78 ¶1-2)

    • Maliko 3:3, 4​—Yesu anadziwa kuti atsogoleriwo ankakhwimitsa kwambiri malamulo okhudza Sabata (jy 78 ¶3)

    • Maliko 3:5​—Yesu anamva “chisoni kwambiri chifukwa cha kuuma mtima kwawo” (mokwiya ndi kumva chisoni kwambiri” mfundo zimene ndikuphunzira pa maliko 3:5, nwtsty)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Maliko 3:28, 29​—Kodi kunyoza mzimu woyera kumatanthauza chiyani, ndipo zotsatira zake zimakhala zotani? (“wanyoza mzimu woyera” “mlandu wa tchimo losatha” mfundo zimene ndikuphunzira pa maliko 3:29, nwtsty)

    • Maliko 4:26-29​—Kodi tikuphunzira chiyani pa fanizo la Yesu la wofesa mbewu amene amagona usiku n’kumadzuka kukacha? (w14 12/15 12-13 ¶6-8)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 3:1-19a

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 36 ¶21-22​—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU