April 30–May 6
MALIKO 5-6
Nyimbo Na. 151 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yesu Ali ndi Mphamvu Zoukitsa Anthu Amene Anamwalira”: (10 min.)
Maliko 5:38—Timalira munthu amene timam’konda akamwalira
Maliko 5:39-41—Yesu ali ndi mphamvu zoukitsa anthu amene “akugona” mu imfa (“sanamwalire ayi, koma akugona” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 5:39, nwtsty)
Maliko 5:42—‘Tidzasangalala kwambiri’ anthu akamadzaukitsidwa m’tsogolo (jy 118 ¶6)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Maliko 5:19, 20—N’chifukwa chiyani Yesu pa nthawiyi anapereka malangizo osiyana ndi omwe ankapereka nthawi zonse? (“ukawauze” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 5:19, nwtsty)
Maliko 6:11—Kodi mawu akuti “sansani fumbi kumapazi anu” amatanthauza chiyani? (“sansani fumbi kumapazi anu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Maliko 6:11, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Maliko 6:1-13
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene. Musonyezeni webusaiti ya jw.org.
Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse loti mugwiritse ntchito komanso funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 36 ¶23-24—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Tizigwiritsa Ntchito Mwaluso Zinthu Zomwe Timagwiritsa Ntchito Pophunzitsa”: (5 min.) Nkhani yokambirana.
Timatonthozedwa Chifukwa Chokhala M’gulu la Yehova: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyoyi. Kenako kambiranani mafunso otsatirawa: Kodi banja la a Pera linakumana ndi mavuto otani? N’chiyani chinawathandiza kuti apirire? Kodi n’chifukwa chiyani tiyenera kupitirizabe kuchita zinthu zokhudza kulambira ngakhale pamene takumana ndi mayesero?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 17 ¶10-18
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 72 ndi Pemphero