April 9-15
MATEYU 27-28
Nyimbo Na. 69 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Tingamvere Bwanji Lamulo Lakuti, Pitani Mukaphunzitse Anthu?”: (10 min.)
Mat. 28:18—Yesu ali ndi ulamuliro waukulu (w04 7/1 8 ¶4)
Mat. 28:19—Yesu anayambitsa ntchito yapadziko lonse yolalikira komanso kuphunzitsa (“mukaphunzitse” “anthu a mitundu yonse” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 28:19, nwtsty)
Mat. 28:20—Tiyenera kuphunzitsa anthu komanso kuwathandiza kuti azitsatira zonse zimene Yesu anaphunzitsa (“ndi kuwaphunzitsa” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 28:20, nwtsty)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Mat. 27:51—Kodi kung’ambika pakati kwa nsalu yotchinga kunkaimira chiyani? (“nsalu yotchinga” “m’nyumba yopatulika” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 27:51, nwtsty)
Mat. 28:7—Kodi mngelo wa Yehova anasonyeza bwanji kuti analemekeza azimayi omwe anapita kumanda a Yesu? (“mukauze ophunzira ake kuti wauka” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mat. 28:7, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mat. 27:38-54
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene.
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Nkhani: (Osapitirira 6 min.) g17.2 14—Mutu: Kodi Yesu Anafera Pamtanda?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kulalikira Komanso Kuphunzitsa N’kofunika Kwambiri Kuti Tipange Ophunzira”: (15 min.) Nkhani Yokambirana. Pokambirana nkhaniyi, onetsani vidiyo yakuti, Pitirizani Kulalikira “Mwakhama”—Mwamwayi Komanso Kunyumba ndi Nyumba komanso yakuti, Pitirizani Kulalikira “Mwakhama”—M’malo Opezeka Anthu Ambiri Komanso Muzithandiza Anthu Kuti Akhale Ophunzira a Yesu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 16 ¶6-17
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 73 ndi Pemphero