Akulandira munthu amene wabwera kumwambo wa Chikumbutso

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU April 2019

Zimene Tinganene

Zitsanzo za ulaliki zofotokoza za imfa ya Yesu Khristu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kusakhala Pabanja ndi Mphatso

Kodi Mkhristu angatani kuti azigwiritsa ntchito nthawi yake mwanzeru pamene sali pabanja?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova ndi Wokhulupirika

Tikakumana ndi mayesero, Yehova amatipatsa zinthu zofunikira kuti tithe kupilira.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kodi Muchikonzekera Bwanji Chikumbutso?

Tonsefe tiyenera kukonzekeretsa mtima wathu. Koma kodi tingachite bwanji zimenezi?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mulungu Adzakhala “Zinthu Zonse kwa Aliyense”

Anthu amene ndi okhulupirika kwa Yehova adzakhala ndi tsogolo labwino kwambiri.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova ndi “Mulungu Amene Amatitonthoza M’njira Iliyonse”

Njira imodzi imene Yehova amagwiritsa ntchito potitonthoza ndi kugwiritsira ntchito abale ndi alongo athu mumpingo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Dziperekeni Kuti Yehova Akuphunzitseni

Yehova, yemwe ndi Mlangizi wathu wamkulu, amatipatsa maphunziro apamwamba kwambiri