April 29–May 5
2 AKORINTO 1-3
Nyimbo Na. 44 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova ndi ‘Mulungu Amene Amatitonthoza M’njira Iliyonse’”: (10 min.)
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Akorinto.]
2 Akor. 1:3—Yehova ndi “Tate wachifundo chachikulu” (w17.07 13 ¶4)
2 Akor. 1:4—Timatha kutonthoza ena chifukwa ifenso timatonthozedwa ndi Yehova (w17.07 15 ¶14)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
2 Akor. 1:22—Kodi odzozedwa amalandira bwanji “chikole” kuchokera kwa mulungu, nanga amadindidwa bwanji “chidindo”? (w16.04 32)
2 Akor. 2:14-16—Kodi Paulo ayenera kuti ankaganizira za chiyani pamene ananena za “chionetsero chonyadirira kupambana”? (w10 8/1 23)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Akor. 3:1-18 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 6)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) bhs 52-53 ¶3-4 (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Dziperekeni Kuti Muphunzitsidwe ndi Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani ndi kukambirana vidiyo yakuti Tinapeza Madalitso Ambiri Chifukwa Chophunzitsidwa ndi Yehova.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 35 ¶12-19
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero