NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU April 2020
Zimene Tinganene
Zitsanzo za zimene tinganene zokhudza cholinga cha Mulungu polenga anthu komanso mmene chidzakwaniritsidwire.
April 6-12
Kodi mungakonzekere bwanji Mwambo Wokumbukira Imfa ya Khristu?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Yakobo ndi Labani Anachita Pangano Lamtendere
Kodi mungatani kuti muzikhala mwamtendere ndi ena?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kodi Mukuyesetsa Kuchita Zonse Zomwe Mungathe Kuti Mupeze Madalitso?
Kodi ndinu okonzeka kuchita zinthu ziti n’cholinga choti Mulungu akudalitseni?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Kodi Chofunika Kwambiri kwa Ine N’chiyani?
Kodi zosankha zanu pa nkhani ya ntchito zimasonyeza kuti chinthu chofunika kwambiri pa moyo wa n’chiyani?
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kuopsa Kocheza ndi Anthu a Makhalidwe Oipa
Kodi mungadziwe bwanji kuti munthu winawake ndi woyenera kumacheza naye kapena ayi?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Chotsani Milungu Yachilendo”
Kodi mungatani kuti muzisangalatsa Yehova ndiponso kupewa zinthu zomwe mizimu yoipa imalimbikitsa kuchita?