Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 31

Yakobo ndi Labani Anachita Pangano Lamtendere

Yakobo ndi Labani Anachita Pangano Lamtendere

31:44-53

N’chifukwa chiyani Yakobo ndi Labani anaunjika mulu wamiyala?

  • Unali ngati umboni kwa anthu onse kuti anachita pangano la mtendere

  • Unkawakumbutsa kuti Yehova akuona ngati akukwaniritsa pangano lawo

Masiku anonso, Yehova amafuna kuti tizikhala mwamtendere ndi abale komanso alongo athu. Kodi zinthu zitatu zotsatirazi zingatithandize bwanji kuti tizikhala mwamtendere ndi ena?