April 20-26
GENESIS 32-33
Nyimbo Na. 21 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mukuyesetsa Kuchita Zonse Zomwe Mungathe Kuti Mupeze Madalitso?”: (10 min.)
Ge 32:24—Yakobo analimbana ndi mngelo (w03 8/15 25 ¶3)
Ge 32:25, 26—Yakobo sanagonje mpaka atalandira madalitso (it-2 190)
Ge 32:27, 28—Yakobo anadalitsidwa chifukwa cha khama lake (it-1 1228)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Ge 32:11, 13-15—Kodi tingatengere bwanji chitsanzo cha Yakobo pa nkhani yokhazikitsa mtendere? (w10 6/15 22 ¶10-11)
Ge 33:20—N’chifukwa chiyani Yakobo anatchula guwa lansembeli kuti “Mulungu, Mulungu wa Isiraeli”? (it-1 980)
Kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ge 32:1-21 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyoyi kenako funsani omvera mafunso otsatirawa: N’chifukwa chiyani tinganene kuti Elise ananena zolondola komanso analalikira mogwira mtima? Kodi Elise ndi Megan anathandizana bwanji kuti alalikire mogwira mtima?
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 12)
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji? kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 16)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kodi Chofunika Kwambiri kwa Ine N’chiyani?”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Musasiye Kukhala ndi Zolinga Zauzimu.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 81
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 12 ndi Pemphero