August 15-21
MASALIMO 102-105
Nyimbo Na. 80 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Amakumbukira Kuti Ndife Fumbi”: (10 min.)
Sal. 103:8-12—Yehova ndi wachifundo kwambiri moti amatikhululukira tikalapa (w13 6/15 20 ndime 14; w12 7/15 16 ndime 17)
Sal. 103:13, 14—Yehova amadziwa zinthu zimene sitingakwanitse kuchita (w15 4/15 26 ndime 8; w13 6/15 15 ndime 16)
Sal. 103:19, 22—Tiziyamikira chifundo chimene Yehova amatisonyeza poyesetsa kuchita zimene amafuna (w10 11/15 25 ndime 5; w07 12/1 21 ndime 1)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Sal. 102:12, 27—Kodi kuganizira kwambiri za ubwenzi wathu ndi Yehova kungatithandize bwanji tikakhumudwa? (w14 3/15 16 ndime 19-21)
Sal. 103:13—N’chifukwa chiyani nthawi zina Yehova sayankha mapemphero athu nthawi yomweyo? (w15 4/15 25 ndime 7)
Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 105:24-45
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) g16.4 tsamba 10-11—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) g16.4 tsamba 10-11—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 164-166 ndime 3-4—Muthandizeni kuona mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’ndimezi.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 91
Osaiwala Zinthu Zonse Zimene Yehova Wakuchitirani (Sal. 103:1-5): (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yamutu wakuti, Khalidwe Langa Loipa Linanditopetsa. (Imapezeka pa jw.org/ny pamene palembedwa kuti ZOKHUDZA IFEYO > ZIMENE TIMACHITA.) Kenako kambiranani mafunso awa: Kodi tili ndi zifukwa zotani zotamandira Yehova? Kodi tikuyembekezera madalitso otani chifukwa cha ubwino wa Yehova?
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 4 ndime 16-31 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 41.
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 131 ndi Pemphero