August 22-28
MASALIMO 106-109
Nyimbo Na. 2 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muziyamikira Yehova”: (10 min.)
Sal. 106:1-3—Yehova ndi woyenera kumuthokoza (w15 1/15 8 ndime 1; w02 6/1 18 ndime 19)
Sal. 106:7-14, 19-25, 35-39—Aisiraeli anasiya kuthokoza Yehova ndipo sanakhalenso okhulupirika (w15 1/15 8-9 ndime 2-3; w01 6/15 13 ndime 1-3)
Sal. 106:4, 5, 48—Tili ndi zifukwa zambiri zothokozera Yehova (w11 10/15 5 ndime 7; w03 12/1 15-16 ndime 3-6)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Sal. 109:8—Kodi Mulungu anakonzeratu zoti Yudasi apereke Yesu kuti ulosi ukwaniritsidwe? (w00 12/15 24 ndime 20; it-1-E 857-858)
Sal. 109:31—Kodi Yehova amaima bwanji “kudzanja lamanja la munthu wosauka”? (w06 9/1 14 ndime 8)
Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Sal. 106:1-22
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) ll 6—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) ll 7—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 178-179 ndime 14-16—Muthandizeni wophunzirayo kuona mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’ndimezi.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 94
Yehova Adzatisamalira (Sal. 107:9): (15 min.) Nkhani yokambirana. Yambani ndi kuonetsa vidiyo yakuti, Yehova Adzatisamalira. (Pitani pamene alemba kuti MAVIDIYO ENA > BANJA.) Pemphani omvera kuti afotokoze zimene tikuphunzirapo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 5 ndime 1-13.
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 149 ndi Pemphero