Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

August 8-14

MASALIMO 92-101

August 8-14
  • Nyimbo Na. 28 ndi Pemphero

  • Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Tsamba loyamba la g16.4—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Tsamba loyamba la g16.4—Siyani funso loti mudzakambirane ulendo wotsatira.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bh 161-162 ndime 18-19—Thandizani wophunzirayo kuti aone mmene angagwiritsire ntchito mfundo za m’ndimezi.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 90

  • Achikulire—Ndinu Ofunika Kwambiri (Sal. 92:12-15): (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yamutu wakuti, Achikulire—Ndinu Ofunika Kwambiri. (Pitani pamene alemba kuti MAVIDIYO ENA > BAIBULO.) Kenako funsani abale ndi alongo kuti afotokoze zomwe tikuphunzirapo. Pemphani abale ndi alongo achikulire kuti azithandiza achinyamata kusankha zinthu mwanzeru komanso aziwafotokozera zomwe anakumana nazo pa moyo wawo. Limbikitsani achinyamata kuti azipempha achikulire kuti aziwathandiza maganizo akamasankha zinthu zofunika kwambiri.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 4 ndime 1-15, komanso bokosi patsamba 39.

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero