Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

August 27–​September 2

Luka 23-24

August 27–​September 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Muzikhala Okonzeka Kukhululukira Ena”: (10 min.)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Luka 23:31​—Kodi n’kutheka kuti Yesu ankatanthauza chiyani pavesili? (“pamene mtengo uli wauwisi, . . . mtengowo ukadzauma” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 23:31, nwtsty)

    • Luka 23:33​—Kodi pali umboni wotani wosonyeza kuti misomali inkagwiritsidwa ntchito popachika munthu pamtengo? (“Msomali M’fupa Lachidendene” zithunzi ndi mavidiyo pa Luka 23:33, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 23:1-16

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha zimene tinganene. Kenako gawirani buku kapena chilichonse chimene chili m’gulu la Zinthu Zomwe Timagwiritsa Ntchito Pophunzitsa, chomwe chili ndi nkhani yomwe ingathandize mwininyumbayo.

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse ndipo gawirani buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu.

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) fg phunziro 4 ¶3-4

MOYO WATHU WACHIKHRISTU