Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

August 6-​12

Luka 17-18

August 6-​12

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • Muzisonyeza Kuyamikira”: (10 min.)

    • Luka 17:11-14​—Yesu anachiritsa anthu 10 akhate (“amuna 10 akhate” “Pitani mukadzionetse kwa ansembe” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 17:12, 14, nwtsty)

    • Luka 17:15, 16​—Munthu mmodzi yekha ndi amene anabwerera kukathokoza kwa Yesu

    • Luka 17:17, 18​—Nkhani imeneyi ikutithandiza kuona kufunika kosonyeza kuyamikira (w08 8/1 14-15 ¶9-10)

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Luka 17:7-10​—Kodi mfundo yaikulu mu fanizo la Yesu palembali ndi yotani? (“opanda pake” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 17:10, nwtsty)

    • Luka 18:8​—Kodi ndi chikhulupiriro chotani chimene Yesu ankanena palembali? (“chikhulupiriro” mfundo zimene ndikuphunzira pa Luka 18:8, nwtsty)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Luka 18:24-43

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU