Nyimbo Na. 99 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Uike Akulu”: (10 min.)
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Tito.]
Tito 1:5-9—Oyang’anira madera amaika abale omwe akwaniritsa ziyeneretso za m’Malemba kuti akhale akulu (w14 11/15 28-29)
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Filimoni.]
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Tito 1:12—N’chifukwa chiyani tinganene kuti lembali silikulimbikitsa tsankho? (w89 5/15 31 ¶5)
Filim. 15, 16—N’chifukwa chiyani Paulo sanapemphe Filimoni kuti amasule Onesimo? (w08 10/15 31 ¶5)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Tito 3:1-15 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 3)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 12)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musiyireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Achinyamata, Mukhale ‘Odzipereka pa Ntchito Zabwino’”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Achinyamata Amene Akulemekeza Yehova.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 46
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 102 ndi Pemphero