August 26–September 1
AHEBERI 4-6
Nyimbo Na. 5 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yesetsani Kuti Mulowe Mumpumulo wa Mulungu”: (10 min.)
Aheb. 4:1, 4—Kodi tsiku la mpumulo wa Mulungu n’chiyani? (w11 7/15 24-25 ¶3-5)
Aheb. 4:6—Muzimvera Yehova (w11 7/15 25 ¶6)
Aheb. 4:9-11—Musamangoyendera maganizo anu (w11 7/15 28 ¶16-17)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Aheb. 4:12—Kodi “mawu a Mulungu” amene akutchulidwa palembali ndi ati? (w16.09 13)
Aheb. 6:17, 18—Kodi “zinthu ziwiri zosasinthika” zimene zatchulidwa palembali ndi ziti? (it-1 1139 ¶2)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Aheb. 5:1-14 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza wachiwiri. (th phunziro 6)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) lvs 228-229 ¶7-8 (th phunziro 12)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Ntchito Zabwino Zimene Yehova Sangaziiwale”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kodi Mungakonde Kutumikira pa Beteli?.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 48
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 118 ndi Pemphero