August 5-11
2 Timoteyo 1-4
Nyimbo Na. 150 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha”: (10 min.)
[Onerani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Timoteyo.]
2 Tim. 1:7—Muziyesetsa kukhala ‘oganiza bwino’ mukakumana ndi mayesero (w09 5/15 15 ¶9)
2 Tim. 1:8—Musamachite manyazi ndi uthenga wabwino (w03 3/1 9 ¶7)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
2 Tim. 2:3, 4—Kodi tingatani kuti tisamachite nawo kwambiri “zamalonda zimene anthu wamba amachita”? (w17.07 10 ¶13)
2 Tim. 2:23—Kodi tingakane bwanji “mafunso opusa ndi opanda nzeru”? (w14 7/15 14 ¶10)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Tim. 1:1-18 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Mafanizo Abwino, kenako kambiranani phunziro 8 m’kabuku ka Kuphunzitsa.
Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w14 7/15 13 ¶3-7—Mutu: Kodi Anthu a Yehova Amakana Bwanji “Kuchita Zosalungama”? (th phunziro 7)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muzicheza ndi Anthu Amene Amakonda Yehova”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Muzipewa Kugwirizana ndi Anthu a Makhalidwe Oipa.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 45
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 55 ndi Pemphero