December 19-25
YESAYA 11-16
Nyimbo Na. 143 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Dziko Lapansi Lidzadzaza ndi Anthu Odziwa Yehova”: (10 min.)
Yes. 11:3-5—Chilungamo chidzakhalapo mpaka kalekale (ip-1 160-161 ¶9-11)
Yes. 11:6-8—Anthu azidzakhala mwamtendere ndi zinyama (w12 9/15 9-10 ¶8-9)
Yes. 11:9—Anthu onse adzaphunzira zimene Yehova amafuna (w16.06 8 ¶9; w13 6/1 7)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Yes. 11:1, 10—Kodi Yesu Khristu angakhale bwanji nthambi yotuluka “pachitsa cha Jese” ndiponso “muzu wa Jese”? (w06 12/1 9 ¶6)
Yes. 13:17—N’chifukwa chiyani Baibulo limanena kuti Amedi ankaona kuti siliva si kanthu komanso sankasangalala ndi golide? (w06 12/1 10 ¶10)
Kodi ndaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo ziti zimene ndaphunzira pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ndingazigwiritse ntchito mu utumiki?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yes. 13:17-22; 14:1-8
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yobu 34:10—Kuphunzitsa Choonadi.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Mlal. 8:9; 1 Yoh. 5:19—Kuphunzitsa Choonadi.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) lv 54 ¶9—Sonyezani mmene tingafikire pamtima wophunzira wathu.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 24
“Zimene Mulungu Amatiphunzitsa Zimatithandiza Kuti Tisakhale Atsankho”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti, Johny ndi Gideon: Anali Khoswe ndi Mphaka Koma Pano Ndi Ogwirizana.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) ia mutu 13 ¶13-25 komanso Mfundo Zofunika Kuziganizira patsamba 114
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 151 ndi Pemphero
Kumbukirani: Muyenera kuika nyimboyi kuti onse amvetsere, kenako muibwerezenso kuti onse aimbe nawo.