Akuimba nyimbo pa kulambira kwa pabanja ku South Africa

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU December 2018

Zimene Tinganene

Zitsanzo za zimene tinganene zokhudza cholinga cha mulungu polenga anthu komanso zimene akutilonjeza m’tsogolomu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Munthu Amene Ankazunza Akhristu Anakhala Mkhristu Wakhama

Ngati mukuphunzira Baibulo koma simunabatizidwe, kodi mungakonde kutsanzira Saulo n’kuyamba kuchita mogwirizana ndi zimene mwaphunzira?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Baranaba ndi Paulo Ankathandiza Anthu Kukhala Ophunzira M’madera Akutali Kwambiri

Baranaba ndi Paulo anagwira ntchito mwakhama pothandiza anthu ofatsa kuti akhale Akhristu.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Muzithandiza Anthu Amene Ali ndi “Maganizo Abwino” Kuti Akhale Ophunzira

Kodi timagwira ntchito bwanji ndi Yehova tikamathandiza anthu kuti akhale ophunzira?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anasankha Zochita Pogwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu

Kodi tikuphunzira chiyani pa nkhani yokhudza mmene nkhani yamdulidwe inathetsedwera?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Tizitamanda Yehova Mosangalala Poimba Nyimbo

Kodi timapindula bwanji tikamaimba nyimbo za Ufumu?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzitsanzira Mtumwi Paulo pa Nkhani Yolalikira Komanso Kuphunzitsa

Kodi tingatsanzire bwanji Paulo tikamalalikira?

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Mukhale Tcheru ndi Kuyang’anira Gulu Lonse la Nkhosa”

Akulu amadyetsa, kuteteza, komanso kusamalira nkhosa, chifukwa amakumbukira kuti nkhosa iliyonse inagulidwa ndi magazi a mtengo wapatali a Yesu.