December 10-16
MACHITIDWE 12-14
Nyimbo Na. 60 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Baranaba ndi Paulo Ankathandiza Anthu Kukhala Ophunzira M’madera Akutali Kwambiri”: (10 min.)
Mac. 13:2, 3—Yehova anasankha Baranaba ndi Saulo kuti agwire ntchito yapadera (bt 86 ¶4)
Mac. 13:12, 48; 14:1—Ntchito yawo inathandiza kuti anthu ambiri akhale Akhristu (bt 95 ¶5)
Mac. 14:21, 22—Baranaba ndi Paulo analimbikitsa ophunzira atsopanowo (w14 9/15 13 ¶4-5)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Mac. 12:21-23—Kodi zimene zinachitikira Herode zikutiphunzitsa chiyani? (w08 5/15 32 ¶7)
Mac. 13:9—N’chifukwa chiyani Saulo ‘ankatchedwanso Paulo’? (“Saulo, wotchedwanso Paulo” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mac. 13:9, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mac. 12:1-17
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsirani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba.
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Nkhani: (Osapitirira 6 min.) bt 78-79 ¶8-9—Mutu: Muzipempherera Okhulupirira Anzanu.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Muzithandiza Anthu Amene Ali ndi ‘Maganizo Abwino’ Kuti Akhale Ophunzira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti, Yehova Mulungu Adzakuthandizani .
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 17
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 86 ndi Pemphero