Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Paulo ndi Baranaba ali kwa Serigio Paulo

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 12-14

Baranaba ndi Paulo Ankathandiza Anthu Kukhala Ophunzira M’madera Akutali Kwambiri

Baranaba ndi Paulo Ankathandiza Anthu Kukhala Ophunzira M’madera Akutali Kwambiri

13:12, 48; 14:1, 21, 22

Baranaba ndi Paulo anagwira ntchito mwakhama pothandiza anthu kuti akhale Akhristu ngakhale kuti ankatsutsidwa kwambiri

  • Ankalalikira anthu a mitundu yosiyanasiyana

  • Ankalimbikitsa ophunzira atsopano kuti “akhalebe m’chikhulupiriro”