December 17-23
MACHITIDWE 15-16
Nyimbo Na. 96 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Anasankha Zochita Pogwiritsa Ntchito Mawu a Mulungu”: (10 min.)
Mac. 15:1, 2—Nkhani yamdulidwe inkafuna kugawanitsa mpingo wachikhristu womwe unangoyamba kumene (bt 102-103 ¶8)
Mac. 15:13-20—Bungwe lolamulira linasankha zochita pa nkhaniyi pogwiritsa ntchito Malemba (w12 1/15 5 ¶6-7)
Mac. 15:28, 29; 16:4, 5—Zimene bungwe lolamulira linasankha pa nkhaniyi zinachititsa kuti mipingo ikhale yolimba (bt 123 ¶18)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Mac. 16:6-9—Kodi nkhaniyi ikutiphunzitsa chiyani pa nkhani yowonjezera utumiki wathu? (w12 1/15 10 ¶8)
Mac. 16:37—Kodi mtumwi Paulo anagwiritsira ntchito bwanji ufulu wake wokhala nzika ya Roma popititsa patsogolo uthenga wabwino? (“ndife Aroma” mfundo zimene ndikuphunzira pa Mac. 16:37, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Mac. 16:25-40
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire pa nkhani inayake yomwe anthu a m’gawo lanu amatsutsa kawirikawiri.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Musonyezeni ndi kukambirana mfundo za m’vidiyo yakuti N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? (koma musaonetse vidiyoyi)
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Wachiwiri: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Tizitamanda Yehova Mosangalala Poimba Nyimbo”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Ana Anatamanda Yehova Poimba Nyimbo. Pomaliza nkhaniyi, pemphani onse kuti aimirire n’kuimbira limodzi vidiyo ya Nyimbo 084 Timadzipereka.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 18
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 123 ndi Pemphero