Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 17-18

Muzitsanzira Mtumwi Paulo pa Nkhani Yolalikira Komanso Kuphunzitsa

Muzitsanzira Mtumwi Paulo pa Nkhani Yolalikira Komanso Kuphunzitsa

17:2, 3, 17, 22, 23

Kodi tingatsanzire bwanji Paulo?

  • Tizigwiritsa ntchito Malemba tikamakambirana ndi anthu komanso kumasintha ulaliki wathu kuti ugwirizane ndi anthu amene takumana nawo

  • Tizilalikira kumalo komanso pa nthawi imene tingakumane ndi anthu ambiri

  • Tizichita zinthu mwaluso poyesetsa kudziwa zimene anthu amakhulupirira n’kugwiritsa ntchito zimenezo poyamba kukambirana nawo