December 2-8
Chivumbulutso 7-9
Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Khamu Lalikulu la Anthu Likudalitsidwa ndi Yehova”: (10 min.)
Chiv. 7:9—“Khamu lalikulu” linaimirira pamaso pa mpando wachifumu (it-1 997 ¶1)
Chiv. 7:14—Khamu lalikulu lidzapulumuka “chisautso chachikulu” (it-2 1127 ¶4)
Chiv. 7:15-17—Khamu lalikulu lidzakhala padziko lapansi ndipo lidzadalitsidwa kwambiri (it-1 996-997)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Chiv. 7:1—Kodi ‘angelo anayi omwe anaimirira m’makona anayi a dziko lapansi’ komanso “mphepo zinayi” zikuimira chiyani? (re 115 ¶4)
Chiv. 9:11—Kodi “mngelo wa phompho” ndi ndani? (it-1 12)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 7:1-12 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kuwerenga Komanso Kuphunzitsa Mwaluso: (10 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kulankhula Mwachikondi Komanso Mokoma Mtima, kenako kambiranani phunziro 12 m’kabuku ka Kuphunzitsa.
Nkhani: (Osapitirira 5 min.) w16.01 25-26 ¶12-16—Mutu: N’chifukwa Chiyani Sitiyenera Kuda Nkhawa ndi Kuwonjezereka kwa Anthu Odya Zizindikiro Komwe Kwachitika M’zaka Zapitazi? (th phunziro 6)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (8 min.)
Zimene Gulu Lathu Lachita: (7 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 62
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 31 ndi Pemphero