Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

December 30, 2019–January 5, 2020

CHIVUMBULUTSO 20-22

December 30, 2019–January 5, 2020

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 3 min.) Sankhani lemba lililonse. M’patseni kapepala komuitanira kumisonkhano yathu. (th phunziro 3)

  • Ulendo Wobwereza Wachitatu: (Osapitirira 4 min.) Sankhani lemba lililonse. M’patseni buku kapena kabuku kamene timagwiritsa ntchito pophunzira ndi anthu. (th phunziro 9)

  • Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) jl phunziro 12 (th phunziro 6)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 57

  • Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki​—Muzisintha Ulaliki Wanu: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 66

  • Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)

  • Nyimbo Na. 94 ndi Pemphero