Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

December 9-15

CHIVUMBULUTSO 10-12

December 9-15

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • ‘Mboni Ziwiri’ Zinaphedwa Koma Zinakhalanso ndi Moyo”: (10 min.)

    • Chiv. 11:3​—“Mboni ziwiri” zinanenera kwa masiku 1,260 (w14 11/15 30)

    • Chiv. 11:7​—Mbonizi zinaphedwa ndi “chilombo”

    • Chiv. 11:11​—“Mboni ziwiri” zija zinakhalanso ndi moyo patadutsa “masiku atatu ndi hafu”

  • Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)

    • Chiv. 10:9, 10​—Kodi uthenga umene Yohane analandira unakhala bwanji wowawa komanso wotsekemera? (it-2 880-881)

    • Chiv. 12:1-5​—Kodi mavesi amenewa anakwaniritsidwa bwanji? (it-2 187 ¶7-9)

    • Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

    • Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

  • Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 10:1-11 (th phunziro 10)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

MOYO WATHU WACHIKHRISTU