December 21-27
LEVITIKO 14-15
Nyimbo Na. 122 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Timafunika Kukhala Oyera Kuti Tizilambira Mulungu Movomerezeka”: (10 min.)
Le 15:13-15—Amuna ankafunika kudziyeretsa akadetsedwa (it-1 263)
Le 15:28-30—Akazi ankafunika kudziyeretsa akadetsedwa (it-2 372 ¶2)
Le 15:31—Yehova amafuna kuti anthu amene amamulambira azikhala oyera (it-1 1133)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Le 14:14, 17, 25, 28—Kodi tingaphunzire chiyani pa zimene wakhate ankafunika kuchita kuti akhale woyera? (it-1 665 ¶5)
Le 14:43-45—Kodi lamulo lokhudza khate loopsa m’nyumba linkaphunzitsa Aisiraeli mfundo iti yokhudza Yehova? (g 1/06 14, bokosi)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Le 14:1-18 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako perekani magazini yokhudza nkhani imene mwininyumbayo anayambitsa. (th phunziro 16
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi a Mboni za Yehova ndi Anthu Otani? kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 11)
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 5 min.) fg phunziro 11 ¶6-7 (th phunziro 19)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Tizigwiritsabe Ntchito Magazini”: (10 min.) Nkhani yokambirana.
Zimene Gulu Lathu Lachita: (5 min.) Onerani vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya December.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (Osapitirira 30 min.) jy mutu 113
Mawu Omaliza (Osapitirira 3 min.)
Nyimbo Na. 84 ndi Pemphero